Yoswa 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Dzuwa likulowa, Yoswa analamula kuti atsitse mafumuwo pamitengoyo+ n’kuwaponyera m’phanga limene anabisalamo lija, ndipo anthuwo anachitadi zimenezi. Kenako anaika miyala ikuluikulu pakhomo la phangalo, yomwe ilipobe mpaka lero. 1 Mafumu 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyumbayo anaimanga ndi miyala yosema+ kale, ndipo kulira kwa nyundo, nkhwangwa, kapena zida zilizonse zachitsulo sikunamveke m’nyumbayo+ pamene anali kuimanga.
27 Dzuwa likulowa, Yoswa analamula kuti atsitse mafumuwo pamitengoyo+ n’kuwaponyera m’phanga limene anabisalamo lija, ndipo anthuwo anachitadi zimenezi. Kenako anaika miyala ikuluikulu pakhomo la phangalo, yomwe ilipobe mpaka lero.
7 Nyumbayo anaimanga ndi miyala yosema+ kale, ndipo kulira kwa nyundo, nkhwangwa, kapena zida zilizonse zachitsulo sikunamveke m’nyumbayo+ pamene anali kuimanga.