Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 14:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ana ake amalemekezedwa, koma iye sadziwa zimenezo.+

      Iwo amakhala opanda pake, koma iye sawaganizira.

  • Mlaliki 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndani angadziwe zabwino zimene munthu angachite pa moyo wake,+ masiku onse a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Pakuti ndani angamuuze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?+

  • Mlaliki 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo chitsiru chimalankhula mawu ambiri.+

      Munthu sadziwa chimene chidzachitike, ndipo ndani angamuuze zimene zidzachitike iye atafa?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena