Genesis 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Yehova Mulungu anati: “Si bwino kuti munthu akhale yekha. Ndimupangira womuthandiza, monga mnzake womuyenerera.”+ 1 Samueli 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Yonatani mwana wa Sauli ananyamuka ndi kupita kwa Davide ku Horesi, kuti akalimbikitse+ Davide kudalira Mulungu.+ Miyambo 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chitsulo chimanola chitsulo chinzake. Momwemonso munthu amanola munthu mnzake.+ Machitidwe 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene anali kutumikira+ Yehova ndi kusala kudya, mzimu woyera unati: “Mwa anthu onse, mundipatulire Baranaba ndi Saulo+ kuti agwire ntchito imene ndinawaitanira.”
18 Kenako Yehova Mulungu anati: “Si bwino kuti munthu akhale yekha. Ndimupangira womuthandiza, monga mnzake womuyenerera.”+
16 Tsopano Yonatani mwana wa Sauli ananyamuka ndi kupita kwa Davide ku Horesi, kuti akalimbikitse+ Davide kudalira Mulungu.+
2 Pamene anali kutumikira+ Yehova ndi kusala kudya, mzimu woyera unati: “Mwa anthu onse, mundipatulire Baranaba ndi Saulo+ kuti agwire ntchito imene ndinawaitanira.”