1 Samueli 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Yonatani mwana wa Sauli ananyamuka ndi kupita kwa Davide ku Horesi, kuti akalimbikitse+ Davide kudalira Mulungu.+
16 Tsopano Yonatani mwana wa Sauli ananyamuka ndi kupita kwa Davide ku Horesi, kuti akalimbikitse+ Davide kudalira Mulungu.+