1 Samueli 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo mtumiki wakeyo anamuuza kuti: “Chita zimene mtima wako ukufuna. Tiye kulikonse kumene ukufuna. Ine ndili nawe limodzi kuti ndichite zofuna za mtima wako.”+
7 Pamenepo mtumiki wakeyo anamuuza kuti: “Chita zimene mtima wako ukufuna. Tiye kulikonse kumene ukufuna. Ine ndili nawe limodzi kuti ndichite zofuna za mtima wako.”+