Genesis 41:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Farao anatuma anthu kukatenga Yosefe+ kundendeko,+ kuti abwere naye mofulumira. Choncho Yosefeyo anameta bwinobwino,+ kenako anasintha zovala+ n’kukaonekera pamaso pa Farao. Genesis 41:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Iweyo ukhala woyang’anira nyumba yanga,+ ndipo anthu anga onse azimvera iweyo.+ Ine ndikhala wokuposa pa ufumu wokha.”+
14 Tsopano Farao anatuma anthu kukatenga Yosefe+ kundendeko,+ kuti abwere naye mofulumira. Choncho Yosefeyo anameta bwinobwino,+ kenako anasintha zovala+ n’kukaonekera pamaso pa Farao.
40 Iweyo ukhala woyang’anira nyumba yanga,+ ndipo anthu anga onse azimvera iweyo.+ Ine ndikhala wokuposa pa ufumu wokha.”+