-
Machitidwe 17:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndipotu nzika zonse za mu Atene ndi alendo ogonera kumeneko, anali kuthera nthawi yawo yonse yopuma akufotokoza kapena kumvetsera nkhani yatsopano.
-