2 Mafumu 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atapita kuti akam’tenge kukamuika m’manda, sanapezepo chilichonse. Iwo anangopezapo mutu, mapazi, ndi zikhatho zake. +
35 Atapita kuti akam’tenge kukamuika m’manda, sanapezepo chilichonse. Iwo anangopezapo mutu, mapazi, ndi zikhatho zake. +