Yobu 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Bwanji sindinafere m’chiberekero?+Bwanji sindinamwalire nditangotuluka m’mimba? Salimo 58:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Woipayo amayenda ngati nkhono imene ikusungunuka.Iwo sadzaona dzuwa ngati mwana wa mayi amene wapita padera.+
8 Woipayo amayenda ngati nkhono imene ikusungunuka.Iwo sadzaona dzuwa ngati mwana wa mayi amene wapita padera.+