1 Mafumu 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atatero, anamuuza Yerobowamu kuti: “Tengapo zidutswa 10, pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wati, ‘Ndikung’amba ufumuwu kuuchotsa m’manja mwa Solomo, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+ 1 Mafumu 11:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Masiku onse amene Solomo analamulira Isiraeli yense ku Yerusalemu anakwana zaka 40.+ Mlaliki 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mawu a wosonkhanitsa anthu,+ mwana wa Davide, mfumu ya ku Yerusalemu.+
31 Atatero, anamuuza Yerobowamu kuti: “Tengapo zidutswa 10, pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wati, ‘Ndikung’amba ufumuwu kuuchotsa m’manja mwa Solomo, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+