Yesaya 38:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu wamoyo, amene akupuma, ndi amene angakutamandeni,+Ngati mmene ineyo ndikuchitira lero.+Bambo akhoza kuphunzitsa+ ana ake za kukhulupirika kwanu. Mateyu 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma mayiyo anati: “Inde Ambuye, komatu tiagalu timadya nyenyeswa zakugwa patebulo la ambuye awo.”+
19 Munthu wamoyo, amene akupuma, ndi amene angakutamandeni,+Ngati mmene ineyo ndikuchitira lero.+Bambo akhoza kuphunzitsa+ ana ake za kukhulupirika kwanu.
27 Koma mayiyo anati: “Inde Ambuye, komatu tiagalu timadya nyenyeswa zakugwa patebulo la ambuye awo.”+