10 N’chifukwa chake ndikadzabwera, ndidzaulula ntchito zake zimene akupitirizabe kuchita.+ Iye amatinenera zamwano,+ komanso chifukwa chosakhutira ndi zinthu zimenezi, iye salandira abalewo+ mwaulemu, ndipo amene amafuna kulandira+ abalewo, amawatsekereza+ ndi kuwachotsa+ mumpingo.