Miyambo 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nzeru za munthu wochenjera ndizo kuzindikira njira imene akuyendamo,+ koma kuganiza mopusa kwa zitsiru ndi chinyengo.+ Mateyu 25:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Adzaika nkhosa kudzanja lake lamanja,+ koma mbuzi adzaziika kumanzere kwake.+ Luka 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mwachitsanzo, ndani wa inu amene akafuna kumanga nsanja sayamba wakhala pansi ndi kuwerengera ndalama zimene adzawononge,+ kuti aone ngati ali ndi ndalama zokwanira kumalizira nsanjayo?
8 Nzeru za munthu wochenjera ndizo kuzindikira njira imene akuyendamo,+ koma kuganiza mopusa kwa zitsiru ndi chinyengo.+
28 Mwachitsanzo, ndani wa inu amene akafuna kumanga nsanja sayamba wakhala pansi ndi kuwerengera ndalama zimene adzawononge,+ kuti aone ngati ali ndi ndalama zokwanira kumalizira nsanjayo?