Miyambo 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 N’chifukwa chiyani munthu wopusa ali ndi njira yopezera nzeru,+ chonsecho alibe zolinga zabwino?*+ Mlaliki 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo chitsiru chimalankhula mawu ambiri.+ Munthu sadziwa chimene chidzachitike, ndipo ndani angamuuze zimene zidzachitike iye atafa?+ Mateyu 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Kenako adzauza a kumanzere kwake kuti, ‘Chokani pamaso panga+ inu otembereredwa. Pitani kumoto wosatha+ wokolezedwera Mdyerekezi ndi angelo ake.+
16 N’chifukwa chiyani munthu wopusa ali ndi njira yopezera nzeru,+ chonsecho alibe zolinga zabwino?*+
14 Ndipo chitsiru chimalankhula mawu ambiri.+ Munthu sadziwa chimene chidzachitike, ndipo ndani angamuuze zimene zidzachitike iye atafa?+
41 “Kenako adzauza a kumanzere kwake kuti, ‘Chokani pamaso panga+ inu otembereredwa. Pitani kumoto wosatha+ wokolezedwera Mdyerekezi ndi angelo ake.+