Miyambo 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+ Miyambo 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Milomo ya munthu wopusa imalowa mu mkangano,+ ndipo pakamwa pake pamaitana zikwapu.+ 1 Petulo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa chakuti simukupitiriza kuthamanga nawo limodzi m’chithaphwi cha makhalidwe oipa,+ anthu a m’dzikoli sakumvetsa, choncho amakunyozani.+
23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+
4 Chifukwa chakuti simukupitiriza kuthamanga nawo limodzi m’chithaphwi cha makhalidwe oipa,+ anthu a m’dzikoli sakumvetsa, choncho amakunyozani.+