1 Samueli 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Poyankha Sauli anati: “Ndachimwa.+ Bwerera mwana wanga Davide, pakuti sindidzakuvulaza chifukwa moyo wanga wakhala wamtengo wapatali+ kwa iwe lero. Taona, ndachita zinthu mopusa ndipo ndalakwitsa kwambiri.” Yesaya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Amene amagawira anthu anga ntchito, akuwagwiritsa ntchito mwankhanza, ndipo akazi ndi amene akuwalamulira.+ Inu anthu anga, amene akukutsogolerani akukusocheretsani,+ ndipo asokoneza njira yanu.+
21 Poyankha Sauli anati: “Ndachimwa.+ Bwerera mwana wanga Davide, pakuti sindidzakuvulaza chifukwa moyo wanga wakhala wamtengo wapatali+ kwa iwe lero. Taona, ndachita zinthu mopusa ndipo ndalakwitsa kwambiri.”
12 Amene amagawira anthu anga ntchito, akuwagwiritsa ntchito mwankhanza, ndipo akazi ndi amene akuwalamulira.+ Inu anthu anga, amene akukutsogolerani akukusocheretsani,+ ndipo asokoneza njira yanu.+