Salimo 58:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Imene singamve mawu a munthu wamatsenga,+Ngakhale wina wanzeru ataimanga ndi mphamvu zamatsenga.+ Yeremiya 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Inetu ndikutumiza njoka pakati panu, njoka zapoizoni,+ zimene simungaziimbire nyimbo kuti muziseweretse,+ ndipo zidzakulumani ndithu,” watero Yehova.
17 “Inetu ndikutumiza njoka pakati panu, njoka zapoizoni,+ zimene simungaziimbire nyimbo kuti muziseweretse,+ ndipo zidzakulumani ndithu,” watero Yehova.