Miyambo 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zolakalaka za munthu waulesi zidzamupha, chifukwa manja ake amakana kugwira ntchito.+ Miyambo 24:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ukati, “Ndigoneko pang’ono, ndibeko katulo pang’ono, ndipindeko manja pang’ono pogona,”+ Aheberi 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pitirizani kuchita zimenezi kuti musakhale aulesi,+ koma mukhale otsanzira+ anthu amene, mwa chikhulupiriro ndi kuleza mtima, akulandira zinthu zimene Mulungu analonjeza monga cholowa chawo.+
12 Pitirizani kuchita zimenezi kuti musakhale aulesi,+ koma mukhale otsanzira+ anthu amene, mwa chikhulupiriro ndi kuleza mtima, akulandira zinthu zimene Mulungu analonjeza monga cholowa chawo.+