Deuteronomo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti sipadzalephera kukhala wosauka m’dziko lako.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti, ‘Uzikhala wowolowa manja kwa m’bale wako wovutika ndi wosauka m’dziko lanu.’+ Miyambo 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wa diso labwino adzadalitsidwa, chifukwa amapereka chakudya chake kwa munthu wonyozeka.+ Yesaya 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Odala ndinu anthu amene mukubzala mbewu m’mphepete mwa madzi onse,+ ndi kumasula ng’ombe yamphongo ndi bulu.”+
11 Pakuti sipadzalephera kukhala wosauka m’dziko lako.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti, ‘Uzikhala wowolowa manja kwa m’bale wako wovutika ndi wosauka m’dziko lanu.’+
20 “Odala ndinu anthu amene mukubzala mbewu m’mphepete mwa madzi onse,+ ndi kumasula ng’ombe yamphongo ndi bulu.”+