Salimo 133:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zili ngati mame+ a ku Herimoni,+Amene akutsikira pamapiri a ku Ziyoni.+Pakuti Yehova analamula dalitso kukhala kumeneko,+Walamulanso kuti kukhale moyo mpaka kalekale.+
3 Zili ngati mame+ a ku Herimoni,+Amene akutsikira pamapiri a ku Ziyoni.+Pakuti Yehova analamula dalitso kukhala kumeneko,+Walamulanso kuti kukhale moyo mpaka kalekale.+