Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 43:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Tsopano Yosefe anachokapo mofulumira chifukwa anagwidwa chifundo mumtima poona m’bale wakeyo.+ Anafunafuna malo oti akalirire, ndipo analowa m’chipinda chamkati n’kukagwetsa misozi.+

  • 1 Mafumu 3:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Popeza mtima wa mayi yemwe mwana wake anali wamoyoyo unayamba kugunda kwambiri+ chifukwa cha mwana wakeyo,+ nthawi yomweyo anauza mfumuyo kuti: “Pepani+ mbuyanga! Amuna inu, m’patseni mayiyu mwana wamoyoyu. Musamuphe ayi.” Apa n’kuti mayi wina uja akunena kuti: “Mwanayu sakhala wanga kapena wako. Amuna inu, m’duleni!”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena