Nyimbo ya Solomo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wachikondi wangayo, ine ndine wakewake ndipo iye ndi wangawanga.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa.” Yohane 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndine m’busa wabwino.+ M’busa wabwino amataya moyo wake chifukwa cha nkhosa.+ Chivumbulutso 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 chifukwa Mwanawankhosa,+ amene ali pambali pa mpando wachifumu, adzawaweta+ ndi kuwatsogolera ku akasupe a madzi+ a moyo. Ndipo Mulungu adzapukuta misozi yonse m’maso mwawo.”+
3 Wachikondi wangayo, ine ndine wakewake ndipo iye ndi wangawanga.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa.”
17 chifukwa Mwanawankhosa,+ amene ali pambali pa mpando wachifumu, adzawaweta+ ndi kuwatsogolera ku akasupe a madzi+ a moyo. Ndipo Mulungu adzapukuta misozi yonse m’maso mwawo.”+