Salimo 45:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana aakazi+ a mafumu ali m’gulu la akazi ako okondedwa.Mkazi wamkulu wa mfumu+ waima kudzanja lako lamanja atavala zovala zagolide wa ku Ofiri.+ Aefeso 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anatero kuti iyeyo alandire mpingowo uli wokongola ndiponso waulemerero,+ wopanda banga kapena makwinya kapenanso chilichonse cha zinthu zotero, koma kuti ukhale woyera ndi wopanda chilema.+
9 Ana aakazi+ a mafumu ali m’gulu la akazi ako okondedwa.Mkazi wamkulu wa mfumu+ waima kudzanja lako lamanja atavala zovala zagolide wa ku Ofiri.+
27 Anatero kuti iyeyo alandire mpingowo uli wokongola ndiponso waulemerero,+ wopanda banga kapena makwinya kapenanso chilichonse cha zinthu zotero, koma kuti ukhale woyera ndi wopanda chilema.+