Nyimbo ya Solomo 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘Kodi mkazi+ amene akuyang’ana pansi ngati m’bandakuchayu ndani,+ wokongola ngati mwezi wathunthu,+ wosadetsedwa ngati dzuwa lowala,+ wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera?’”+
10 ‘Kodi mkazi+ amene akuyang’ana pansi ngati m’bandakuchayu ndani,+ wokongola ngati mwezi wathunthu,+ wosadetsedwa ngati dzuwa lowala,+ wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera?’”+