Nyimbo ya Solomo 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kwa ine, wachikondi wanga ali ngati duwa lofiirira+ m’minda ya mpesa ya ku Eni-gedi.”+ Nyimbo ya Solomo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Khungu lako lili ngati munda wokongola* wokhala ndi mitengo ya makangaza ya zipatso zabwino kwambiri,+ mitengo ya maluwa ofiirira, mitengo ya nado,+
13 Khungu lako lili ngati munda wokongola* wokhala ndi mitengo ya makangaza ya zipatso zabwino kwambiri,+ mitengo ya maluwa ofiirira, mitengo ya nado,+