Nyimbo ya Solomo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musandiyang’anitsitse chifukwa chakuti ndada, ndi dzuwatu landidetsali. Pakuti ana aamuna a mayi anga anandikwiyira. Choncho anandiika kuti ndiziyang’anira minda ya mpesa moti sindinathe kuyang’anira munda wangawanga wa mpesa.+
6 Musandiyang’anitsitse chifukwa chakuti ndada, ndi dzuwatu landidetsali. Pakuti ana aamuna a mayi anga anandikwiyira. Choncho anandiika kuti ndiziyang’anira minda ya mpesa moti sindinathe kuyang’anira munda wangawanga wa mpesa.+