Nyimbo ya Solomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Bwerera, bwerera iwe Msulami! Bwerera, bwerera kuti tikuone!”+ “Kodi anthu inu mukuona chiyani mwa ine Msulami?”+ “Tikuona ngati tikuonerera gule wa magulu awiri a anthu.” Nyimbo ya Solomo 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Wachikondi wangayo, ine ndine wake,+ ndipo iye akulakalaka ineyo.+
13 “Bwerera, bwerera iwe Msulami! Bwerera, bwerera kuti tikuone!”+ “Kodi anthu inu mukuona chiyani mwa ine Msulami?”+ “Tikuona ngati tikuonerera gule wa magulu awiri a anthu.”