2 Akorinto 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero okondedwanu, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse+ ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi kapena mzimu,+ kwinaku tikukwaniritsa kukhala oyera poopa Mulungu.+ Agalatiya 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 kufatsa ndi kudziletsa.+ Palibe lamulo loletsa zinthu zoterezi.+ 1 Petulo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 poona okha ndi maso awo khalidwe lanu loyera+ ndi ulemu wanu waukulu.
7 Chotero okondedwanu, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse+ ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi kapena mzimu,+ kwinaku tikukwaniritsa kukhala oyera poopa Mulungu.+