Salimo 45:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu idzalakalaka kukongola kwako,+Pakuti ndiyo mbuye wako,+Choncho iweramire.+ Nyimbo ya Solomo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ndiwe wokongola paliponse,+ wokondedwa wanga, ndipo mwa iwe mulibe chilema chilichonse.+