Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 29:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Leya anali ndi maso ofooka, pamene Rakele+ anali chiphadzuwa.+

  • Nyimbo ya Solomo 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Ndiwe wokongola kwabasi,+ wokondedwa wanga. Ndiwe chiphadzuwa. Maso ako ali ngati maso a njiwa+ munsalu yako yophimba kumutuyo.+ Tsitsi lako likuoneka ngati gulu la mbuzi+ zimene zikudumphadumpha potsetsereka kuchokera kudera lamapiri la Giliyadi.+

  • Nyimbo ya Solomo 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Panopa ndili m’tulo koma mtima wanga uli maso.+ Ndikumva wachikondi wanga akugogoda.”+

      “Nditsegulire+ iwe mlongo wanga, wokondedwa wanga, njiwa yanga, iwe wopanda chilema.+ Pakuti m’mutu mwanga mwadzaza mame, ndipo tsitsi langa ladzaza madontho a madzi a usiku.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena