Genesis 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Yakobo anakonda Rakele, ndiye anati: “Ndine wokonzeka kukugwirirani ntchito zaka 7, kuti mudzandipatse Rakele mwana wanu wamng’onoyu.”+ Genesis 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yakobo anagwira ntchito zaka 7 kuti atenge Rakele.+ Koma iye anangoziona zakazo ngati masiku ochepa chabe, chifukwa anam’konda kwambiri mtsikanayo.+
18 Koma Yakobo anakonda Rakele, ndiye anati: “Ndine wokonzeka kukugwirirani ntchito zaka 7, kuti mudzandipatse Rakele mwana wanu wamng’onoyu.”+
20 Yakobo anagwira ntchito zaka 7 kuti atenge Rakele.+ Koma iye anangoziona zakazo ngati masiku ochepa chabe, chifukwa anam’konda kwambiri mtsikanayo.+