Salimo 45:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwe mwana wanga wamkazi, mvetsera ndipo ona ndi kutchera khutu.Uiwale anthu ako ndi nyumba ya bambo ako.+ Yohane 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiponso, ndikapita kukakukonzerani malo, ndidzabweranso+ kudzakutengerani kwathu,+ kuti kumene kuli ineko inunso mukakhale kumeneko.+
10 Iwe mwana wanga wamkazi, mvetsera ndipo ona ndi kutchera khutu.Uiwale anthu ako ndi nyumba ya bambo ako.+
3 Ndiponso, ndikapita kukakukonzerani malo, ndidzabweranso+ kudzakutengerani kwathu,+ kuti kumene kuli ineko inunso mukakhale kumeneko.+