Yesaya 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nkhata yamaluwa yokongola imene maluwa ake akufota,+ yomwe ili pamwamba pa phiri m’chigwa chachonde, idzakhala ngati nkhuyu yoyambirira kucha+ chilimwe chisanafike, imene munthu akaiona amaithyola n’kuimeza msangamsanga. Nahumu 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Malo ako onse okhala ndi mpanda wolimba kwambiri ali ngati mitengo ya mkuyu imene ili ndi nkhuyu zoyambirira kupsa. Munthu akagwedeza mitengoyo, nkhuyu zakezo zimagwera m’kamwa mwa munthu wozidya.+
4 Nkhata yamaluwa yokongola imene maluwa ake akufota,+ yomwe ili pamwamba pa phiri m’chigwa chachonde, idzakhala ngati nkhuyu yoyambirira kucha+ chilimwe chisanafike, imene munthu akaiona amaithyola n’kuimeza msangamsanga.
12 Malo ako onse okhala ndi mpanda wolimba kwambiri ali ngati mitengo ya mkuyu imene ili ndi nkhuyu zoyambirira kupsa. Munthu akagwedeza mitengoyo, nkhuyu zakezo zimagwera m’kamwa mwa munthu wozidya.+