Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nyimbo ya Solomo 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Panopa ndili m’tulo koma mtima wanga uli maso.+ Ndikumva wachikondi wanga akugogoda.”+

      “Nditsegulire+ iwe mlongo wanga, wokondedwa wanga, njiwa yanga, iwe wopanda chilema.+ Pakuti m’mutu mwanga mwadzaza mame, ndipo tsitsi langa ladzaza madontho a madzi a usiku.”+

  • Yeremiya 48:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “‘Inu anthu okhala ku Mowabu, chokani mumzinda ndi kukakhala pathanthwe.+ Khalani ngati njiwa imene imamanga chisa chake pakhomo la dzenje m’matanthwemo.’”+

  • Mateyu 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena