Yesaya 62:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti monga momwe mnyamata amatengera namwali kuti akhale mkazi wake, ana ako aamuna adzakutenga kuti ukhale mkazi wawo.+ Monga momwe mkwati amakhalira wachimwemwe chifukwa cha mkwatibwi,+ Mulungu wako adzakhala ndi chimwemwe chifukwa cha iwe.+
5 Pakuti monga momwe mnyamata amatengera namwali kuti akhale mkazi wake, ana ako aamuna adzakutenga kuti ukhale mkazi wawo.+ Monga momwe mkwati amakhalira wachimwemwe chifukwa cha mkwatibwi,+ Mulungu wako adzakhala ndi chimwemwe chifukwa cha iwe.+