Yesaya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye adzayang’ana padziko lapansi koma adzangoonapo kuzunzika, mdima,+ kuda, nthawi zovuta ndi zakuda bii, zopanda kuwala.+ Maliro 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chisangalalo cha mumtima mwathu chatha. Kuvina kwathu kwasanduka kulira maliro.+
22 Iye adzayang’ana padziko lapansi koma adzangoonapo kuzunzika, mdima,+ kuda, nthawi zovuta ndi zakuda bii, zopanda kuwala.+