Yesaya 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero Ambuye woona, Yehova wa makamu azidzatumizira anthu ake* onenepa nthenda yowondetsa,+ ndipo pansi pa ulemerero wake pazidzangoyaka, ngati kuyaka kwa moto.+ Yesaya 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “M’tsiku limenelo, ulemerero wa Yakobo udzachepa,+ ndipo thupi lake lonenepa lidzaonda.+
16 Chotero Ambuye woona, Yehova wa makamu azidzatumizira anthu ake* onenepa nthenda yowondetsa,+ ndipo pansi pa ulemerero wake pazidzangoyaka, ngati kuyaka kwa moto.+