Amosi 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo amalumbira pa milungu yonama ya ku Samariya,*+ ya ku Dani,+ ndi ya ku Beere-seba.*+ Ndithu, anthu amenewa adzagwa ndipo sadzadzukanso.’”+
14 Iwo amalumbira pa milungu yonama ya ku Samariya,*+ ya ku Dani,+ ndi ya ku Beere-seba.*+ Ndithu, anthu amenewa adzagwa ndipo sadzadzukanso.’”+