Genesis 41:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Farao anatuma anthu kukatenga Yosefe+ kundendeko,+ kuti abwere naye mofulumira. Choncho Yosefeyo anameta bwinobwino,+ kenako anasintha zovala+ n’kukaonekera pamaso pa Farao.
14 Tsopano Farao anatuma anthu kukatenga Yosefe+ kundendeko,+ kuti abwere naye mofulumira. Choncho Yosefeyo anameta bwinobwino,+ kenako anasintha zovala+ n’kukaonekera pamaso pa Farao.