Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 119:165
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 165 Okonda chilamulo chanu amapeza mtendere wochuluka,+

      Ndipo palibe chowakhumudwitsa.+

  • Yesaya 54:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+

  • Yohane 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndikusiyirani mtendere, ndikupatsani mtendere wanga.+ Sindikuupereka kwa inu mmene dziko limauperekera ayi. Mitima yanu isavutike kapena kuchita mantha.

  • Aroma 15:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Mulungu amene amapatsa mtendere akhale ndi nonsenu.+ Ame.

  • Afilipi 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mukatero, mtendere+ wa Mulungu umene umaposa kuganiza mozama kulikonse, udzateteza mitima yanu+ ndi maganizo anu mwa Khristu Yesu.

  • 2 Petulo 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndikufuna kuti mulandire kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere wowonjezereka.+ Kuti muchite zimenezi, mumudziwe molondola+ Mulungu ndi Yesu Ambuye wathu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena