Zefaniya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+ Malaki 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Anthu inu mudzapondaponda anthu oipa. Iwo adzakhala ngati fumbi kumapazi anu pa tsiku limene ndidzachitepo kanthu,”+ watero Yehova wa makamu.
12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+
3 “Anthu inu mudzapondaponda anthu oipa. Iwo adzakhala ngati fumbi kumapazi anu pa tsiku limene ndidzachitepo kanthu,”+ watero Yehova wa makamu.