Salimo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nyamukani,+ inu Yehova. Inu Mulungu, tukulani dzanja lanu.+Musaiwale anthu osautsika.+ Mika 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dzanja lanu lidzakhala pamwamba pa adani anu,+ ndipo adani anu onse adzaphedwa.”+