2 Mafumu 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho wina anapita kutchire kukathyola masamba,+ ndipo anapezako kamtengo koyanga, n’kuthyolapo mphonda zakutchire kudzaza pachovala chake. Atatero anabwera nazo n’kuziduladula. Kenako anazithira mumphika uja, koma iwo sankazidziwa bwinobwino.
39 Choncho wina anapita kutchire kukathyola masamba,+ ndipo anapezako kamtengo koyanga, n’kuthyolapo mphonda zakutchire kudzaza pachovala chake. Atatero anabwera nazo n’kuziduladula. Kenako anazithira mumphika uja, koma iwo sankazidziwa bwinobwino.