Salimo 121:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taonani! Amene akuyang’anira Isiraeli,+Sangawodzere kapena kugona.+ Yesaya 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine sindisintha ngakhale kwa wokalamba,+ ndipo munthu wa imvi ndimamunyamula nthawi zonse.+ Ndithu ineyo ndidzachitapo kanthu+ kuti ndiwatenge, ndiwanyamule ndi kuwapulumutsa.+
4 Ine sindisintha ngakhale kwa wokalamba,+ ndipo munthu wa imvi ndimamunyamula nthawi zonse.+ Ndithu ineyo ndidzachitapo kanthu+ kuti ndiwatenge, ndiwanyamule ndi kuwapulumutsa.+