Yesaya 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti dzanja la Yehova lidzakhazikika paphiri limeneli,+ ndipo Mowabu adzapondedwapondedwa+ pamalo pake ngati mulu wa udzu umene umapondedwapondedwa pamalo opangira manyowa.+ Maliro 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova wandichotsera anthu anga onse amphamvu+ ndi kuwakankhira pambali.Wandiitanitsira msonkhano kuti athyolethyole anyamata anga.+Yehova wapondaponda moponderamo mphesa+ mwa namwali, mwana wamkazi wa Yuda.+
10 Pakuti dzanja la Yehova lidzakhazikika paphiri limeneli,+ ndipo Mowabu adzapondedwapondedwa+ pamalo pake ngati mulu wa udzu umene umapondedwapondedwa pamalo opangira manyowa.+
15 Yehova wandichotsera anthu anga onse amphamvu+ ndi kuwakankhira pambali.Wandiitanitsira msonkhano kuti athyolethyole anyamata anga.+Yehova wapondaponda moponderamo mphesa+ mwa namwali, mwana wamkazi wa Yuda.+