Yesaya 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’chifukwa chake iwo adzalemekeze Yehova+ m’chigawo cha kuwala.*+ M’zilumba zakunyanja adzalemekeza dzina la Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli. Yesaya 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwezi wathunthu wachita manyazi. Dzuwa lowala lachitanso manyazi,+ pakuti Yehova wa makamu wakhala mfumu+ yaulemerero m’phiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu, pamaso pa anthu ake achikulire.+ Yesaya 62:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Udzakhala chisoti chokongola m’dzanja la Yehova,+ ndiponso chisoti chachifumu m’dzanja la Mulungu wako.
15 N’chifukwa chake iwo adzalemekeze Yehova+ m’chigawo cha kuwala.*+ M’zilumba zakunyanja adzalemekeza dzina la Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli.
23 Mwezi wathunthu wachita manyazi. Dzuwa lowala lachitanso manyazi,+ pakuti Yehova wa makamu wakhala mfumu+ yaulemerero m’phiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu, pamaso pa anthu ake achikulire.+
3 Udzakhala chisoti chokongola m’dzanja la Yehova,+ ndiponso chisoti chachifumu m’dzanja la Mulungu wako.