Danieli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 amene analibe chilema chilichonse,+ ooneka bwino, ozindikira zinthu, anzeru,+ odziwa zinthu, omvetsa zinthu mwamsanga,+ amenenso akanatha kutumikira m’nyumba ya mfumu.+ Anawabweretsa kuti awaphunzitse kulemba* ndiponso chinenero cha Akasidi. 1 Akorinto 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’Chilamulo muli mawu akuti: “‘Anthu awa+ ndidzawalankhula m’malilime a alendo,+ ndipo ndidzawalankhula ndi milomo ya anthu achilendo, koma iwo sadzandimverabe,’ watero Yehova.”+
4 amene analibe chilema chilichonse,+ ooneka bwino, ozindikira zinthu, anzeru,+ odziwa zinthu, omvetsa zinthu mwamsanga,+ amenenso akanatha kutumikira m’nyumba ya mfumu.+ Anawabweretsa kuti awaphunzitse kulemba* ndiponso chinenero cha Akasidi.
21 M’Chilamulo muli mawu akuti: “‘Anthu awa+ ndidzawalankhula m’malilime a alendo,+ ndipo ndidzawalankhula ndi milomo ya anthu achilendo, koma iwo sadzandimverabe,’ watero Yehova.”+