Salimo 81:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma anthu anga sanamvere mawu anga.+Ndipo Isiraeli sanasonyeze kuti ndi wofunitsitsa kundimvera.+ Yeremiya 44:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Ife sitimvera mawu amene watiuza m’dzina la Yehova.+
11 Koma anthu anga sanamvere mawu anga.+Ndipo Isiraeli sanasonyeze kuti ndi wofunitsitsa kundimvera.+