Habakuku 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mtunduwu umaseka mafumu monyodola ndipo umaona nduna zapamwamba ngati choseketsa.+ Umasekanso malo alionse okhala ndi mpanda wolimba kwambiri+ ndipo umaunjika dothi kenako n’kulanda malowo.
10 Mtunduwu umaseka mafumu monyodola ndipo umaona nduna zapamwamba ngati choseketsa.+ Umasekanso malo alionse okhala ndi mpanda wolimba kwambiri+ ndipo umaunjika dothi kenako n’kulanda malowo.