Ekisodo 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno anthu onse anali kumva mabingu ndi kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa ndipo anali kuona kung’anima kwa mphezi ndiponso phiri likufuka utsi. Anthuwo atamva ndi kuona zimenezi ananjenjemera ndipo anaimabe patali.+ 1 Mbiri 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola,+ ulemerero,+ ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi za padziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu+ ndi wanu, inu Yehova, ndinunso Wokwezeka monga mutu pa onse.+ Salimo 119:120 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+
18 Ndiyeno anthu onse anali kumva mabingu ndi kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa ndipo anali kuona kung’anima kwa mphezi ndiponso phiri likufuka utsi. Anthuwo atamva ndi kuona zimenezi ananjenjemera ndipo anaimabe patali.+
11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola,+ ulemerero,+ ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi za padziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu+ ndi wanu, inu Yehova, ndinunso Wokwezeka monga mutu pa onse.+
120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+